"The Pilgrim's Progress," Volume 1; In the Manganga Language. for Use in Lake Nyassa District, Central Africa

 
9781231937853:
View all copies of this ISBN edition:
 
 

This historic book may have numerous typos and missing text. Purchasers can usually download a free scanned copy of the original book (without typos) from the publisher. Not indexed. Not illustrated. 1894 edition. Excerpt: ...ndi iwe? Wokul. Koh! Ananyoza kupempera Muhmgu kom.we; adati kupempera ndiko kwa ukapolo, kwa F wa chabe kopanda pache; adati mtima wakuopa kuchimwa suli wamwamna; woang'anira mwini man ache ndi kanchito konse kache kuti asachimwe nako ndiye wokana ufulu wache wa amna akulu adzolowera nawo, ndiye adzasekedwa ndi antu onse. Adatinso kuti akulu amodzi amodzi oka, akulemera amodzi amodzi, anzeru amodzi amodzi oka adali a mtima wanga; etu, iwo omweo sadati choincho kufikira pa kuchita za misala ndi kupusa n ti kutaia zonse zao chifukwa cha chimene palibe wodziwa chimenecho. Ndiponso ananyoza aulendo uno onse a maiko onse ngati a mpawi woka, opanda zopunzira a nzeru zazing'ono. Etu, adandineneza ine choincho zambiri zina, sindidziwa kuzinena tsopano pano; adati chamanyazi kulira ndi kubuulira paknnenera wina mau a Mulungu; cha manyazi kunka kwatu chinsinsi ndi kulira; cha nianyazi kupempa anzatu atikululnkire ife zochimwa zatu zazing'ono ng'ono, ndi kuabwezera zimene tinanyenga iwo. Adanenanso kuti popempera Mulungu, tidzisiana ndi akulu amene amacbimwa ndi kuchita zakwaipa (zoipa zomwe anazichula maina akuzilemekeza). Ndipo tilemekeza antu opanda pache, chifukwa iwo amlemekeza Mulungu chomweoho ndi ife tomwe. Kodi ichi sichili cha manyazi? Adati choincho. Wak. Koma udati chiani kwa iye? Wokul. Ine I Poyamba sindikadziwai chimene ndinene. Etu, anandibvuta ine nako ndinagwa nkope wa manyazi. Ndoto yemwe! Anachita choincho. Etu, akati apambane nane. Koma poganizitsa ndinati antu amafuna zimene kwambiri Mulungu adana nazo. Ndipo ndinati:--Ndoto amene amandiuza za antu zoka sanenai za Mulungu ndi za mau a Mulungu. Ndinanenanso tsiku la kumalizira, ife sitidzanenedwe tikale a moyo pena tife, ndi antu a mpamvu akunyadira, koma ndi nzeru za Mulungu...

"synopsis" may belong to another edition of this title.

(No Available Copies)

Search Books:Create a Want

If you know the book but cannot find it on AbeBooks, we can automatically search for it on your behalf as new inventory is added. If it is added to AbeBooks by one of our member booksellers, we will notify you!

Create a Want